Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #253

Hymn 253 Mbusa wa Israyeli

[V1]
HE CALLS HIS LAMBS
1. Mbusa wa a Israyeli, Wocititsa cidwi;
Imva aitana nkhosa Adzatifukate!

2. Akaitana zimadza, Satonza maina;
Amazidalitsa zonse, Mwinu wa angelo.

3. Tibwera nazo kwa Inu, Tikupatsirani,
Ife tiri anu omwe, Ana’thu ndi anu.

253. Mbusa wa Israyeli

Link copied to clipboard successfully!