Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #204

Hymn 204 Bwera Wosocera! Bwera!

[V1]
WELCOME! WELCOME! WELCOME! 1. M’dziko la alendo, Komwe ukhala,
Imva kuitana, "Mwana wanga!’

[C]

"Bwera wosocera! Bwerera Kwanu!
Wasocera Kutali; Bwera kwanu!’

2. Ku dziko la njala, Wokomokawe
Idza ukondwe, "Mwana wanga!"

3. Siya zanduzo Coka m’matsoka,
Watopa mumtima, "Mwana wanga!"

4. Komo Ndotseguka! Ndiwe wangabe;
Ndikuyang’anabe, "Mwana wanga!"

5. Wasocereratu; Subwera kodi?
Wakhulukidwa, "Mwana wanga!"

6. Gome lilindira, Suiwalika!
Udzadye upume, "Mwana wanga!"

7. Wopanda kwanu’we, Wopereweza,
Ndikukonda iwe, "Mwana wanga!"

204. Bwera Wosocera! Bwera!

Link copied to clipboard successfully!